Numbers 26:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Potsata mabanja ao ana aamuna a Benjamini anali aŵa: Bela anali kholo la banja la Abela. Asibele anali kholo la banja la Aasibele. Ahiramu anali kholo la banja la Aahiramu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana amuna a Benjamini monga mwa mabanja ao ndiwo: Bela, ndiye kholo la banja la Abela; Asibele, ndiye kholo la banja la Aasibele; Ahiramu, ndiye kholo la banja la Aahiramu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Benjamini monga mwa mabanja awo zinali izi: kuchokera mwa Bela, fuko la Abela; kuchokera mwa Asibeli, fuko la Aasibeli; kuchokera mwa Ahiramu, fuko la Ahiramu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana amuna a Benjamini monga mwa mabanja ao ndiwo: Bela, ndiye kholo la banja la Abela; Asibeli, ndiye kholo la banja la Aasibeli; Ahiramu, ndiye kholo la banja la Aahiramu;