Numbers 26:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo ana aamuna a Bela anali Aradi ndi Namani. Aradi anali kholo la banja la Aaradi. Namani anali kholo la banja la Anamani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana amuna a Bela ndiwo Aridi ndi Naamani; Aridi, ndiye kholo la banja la Aaridi; Naamani, ndiye kholo la banja la Anaamani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Bela kupyolera mwa Aridi ndi Naamani zinali izi: kuchokera mwa Aridi, fuko la Aaridi; kuchokera mwa Naamani, fuko la Anaamani;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana amuna a Bela ndiwo Aridi ndi Namani; Aridi, ndiye kholo la banja la Aaridi; Namani, ndiye kholo la banja la Anamani.