Numbers 26:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa, anthu okwanira 45,600, ndiwo anali a m'mabanja a Benjamini, amene adaŵerengedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ndiwo ana a Benjamini monga mwa mabanja ao; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa ndiwo anali mabanja a Benjamini. Amene nawerengedwa analipo 45,600.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ndiwo ana a Benjamini monga mwa mabanja ao; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi.