Numbers 26:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu oŵerengedwa pa mabanja onse a Suhamu adakwanira 64,400.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mabanja onse a Asuhamu monga mwa owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse a fuko la Asuhamu amene anawerengedwa analipo 64,400.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mabanja aose a Asuhamu monga mwa owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana anai.