Numbers 26:45 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana aamuna a Beriya anali aŵa: Hebere anali kholo la banja la Ahebri. Malikiele anali kholo la banja la Amalikiele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Beriya ndiwo: Hebere, ndiye kholo la banja la Ahebere; Malikiele, ndiye kholo la banja la Amalikiele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo kupyolera mwa zidzukulu za Beriya: kuchokera mwa Heberi, fuko la Aheberi; kuchokera mwa Malikieli, fuko la Amalikieli;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Beriya ndiwo: Heberi, ndiye kholo la banja la Aheberi; Malikiyeli, ndiye kholo la banja la Amalikiyeli.