Numbers 26:46 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wamkazi wa Asere anali Sera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo dzina la mwana wamkazi wa Asere ndiye Sera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Aseri anali ndi mwana wamkazi dzina lake Sera)
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo dzina la mwana wamkazi wa Aseri ndiye Sera.