Numbers 26:47 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa, anthu okwanira 53,400, ndiwo adaŵerengedwa pa mabanja a Asere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ndiwo mabanja a ana amuna a Asere monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa ndiwo anali mafuko a Aseri. Onse amene anawerengedwa analipo 53,400.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ndiwo mabanja a ana amuna a Aseri monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai.