Numbers 26:48 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Potsata mabanja ao ana aamuna a Nafutali anali aŵa: Yazeele anali kholo la banja la Ayazeele. Guni anali kholo la banja la Aguni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana amuna a Nafutali monga mwa mabanja ao ndiwo: Yazeele, ndiye kholo la banja la Ayezeele; Guni, ndiye kholo la banja la Aguni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Nafutali mwa mafuko awo zinali izi: kuchokera mwa Yahazeeli, fuko la Ayahazeeli; kuchokera mwa Guni, fuko la Aguni;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana amuna a Nafitali monga mwa mabanja ao ndiwo: Yazeli, ndiye kholo la banja la Ayazeli; Guni, ndiye kholo la banja la Aguni;