Numbers 26:50 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa, anthu okwanira 45,400, ndiwo adaŵerengedwa pa mabanja a Nafutali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ndiwo mabanja a Nafutali, monga mwa mabanja ao; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa ndiwo anali mafuko a Nafutali. Onse amene anawerengedwa analipo 45,400.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ndiwo mabanja a Nafitali, monga mwa mabanja ao; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana anai.