Numbers 26:53 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Uŵagaŵire dziko anthu ameneŵa, kuti likhale choloŵa chao, molingana ndi chiŵerengero cha maina ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko ligawikire iwowa monga mwa kuwerenga kwa maina, likhale cholowa chao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Uwagawire dziko anthu awa kuti likhale cholowa chawo molingana ndi chiwerengero cha mayina awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko ligawikire iwowa monga mwa kuwerenga kwa maina, likhale colowa cao.