Numbers 26:55 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma dzikolo uligaŵe mwamaere. Alandire choloŵa chao potsata kuchuluka kwa maina a mafuko a makolo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma aligawe ndi kuchita maere; cholowa chao chikhale monga mwa maina a mafuko a makolo ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzikolo uligawe pochita maere. Alandire cholowa chawocho potsata mayina a mafuko a makolo awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma aligawe ndi kucita maere; colowa cao cikhale monga mwa maina a mafuko a makolo ao,