Numbers 26:61 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Nadabu ndi Abihu adafa chifukwa adaapereka moto wosaloledwa pamaso pa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Nadabu ndi Abihu adafa, muja anabwera nao moto wachilendo pamaso pa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Nadabu ndi Abihu anafa pamene anapereka nsembe pamaso pa Yehova ndi moto wachilendo).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Nadabu ndi Abihu adafa, muja anabwera nao moto wacilendo pamaso pa Yehova.