Numbers 26:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa, anthu okwanira 43,730, ndiwo anali a m'mabanja a Rubeni, amene adaŵerengedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ndiwo mabanja a Arubeni; owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zitatu kudza mazana asanu ndi awiri mphambu makumi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa anali mafuko a Rubeni: onse amene anawerengedwa analipo 43,730.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ndiwo mabanja a Arubeni; owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zitatu kudza mazana asanu ndi awiri mphambu makumi atatu,