Numbers 27:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo utaliwona, udzamwalira monga momwe adachitira Aroni mbale wako,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Utaliona iwenso udzaitanidwa kunka kwa anthu a mtundu wako, monga anaitanidwa Aroni mbale wako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ukakaliona udzamwalira ngati Aaroni mʼbale wako,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Utaliona iwenso udzaitanidwa kumka kwa anthu a mtundu wako, monga anaitanidwa Aroni mbale wako;