Numbers 27:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akakhala kuti alibe mwana wamkazi, choloŵa chakecho chikhale cha abale ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akapanda kukhala naye mwana wamkazi, mupatse abale ake cholowa chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati alibe mwana wamkazi, muzipereka cholowa chakecho kwa abale ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akapanda kukhala naye mwana wamkazi, mupatse abale ace colowa cace.