Numbers 28:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiponso wa makilogaramu limodzi pa mwanawankhosa aliyense.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
upereke limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi; uzitero ndi anaankhosa asanu ndi awiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kilogalamu imodzi pa mwana wankhosa aliyense mwa ana ankhosa asanu ndi awiri aja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
upereke limodzi la magawo khumi likhale la mwana wa nkhosa mmodzi; uzitero ndi ana a nkhosa asanu ndi awiri;