Numbers 28:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muperekenso tonde mmodzi kuti akhale nsembe yochitira mwambo wopepesera machimo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo, yakutetezera inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muziphatikizapo mbuzi yayimuna monga nsembe yopepesera machimo anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi tonde mmodzi akhale nsembe yaucimo, yakutetezera inu.