Numbers 28:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero pa masiku asanu ndi aŵiri muzipereka tsiku lililonse chakudya cha nsembe yotentha pa moto, yotulutsa fungo lokomera Chauta. Muchipereke kuwonjezera pa nsembe zopsereza za tsiku ndi tsiku zija pamodzi ndi zopereka za chakumwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Momwemo mupereke chakudya cha nsembe yamoto cha fungo lokoma la Yehova, tsiku ndi tsiku, masiku asanu ndi awiri, chakupereka pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yothira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motere muzikonza chakudya cha nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku pa masiku asanu ndi awiri ngati fungo lokomera Yehova. Zimenezi ziziperekedwa kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya nthawi zonse pamodzi ndi nsembe yachakumwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Momwemo mupereke cakudya ca nsembe yamoto ca pfungo lokoma la Yehova, tsiku ndi tsiku, masiku asanu ndi awiri, cakupereka pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yace yothira.