Numbers 28:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiponso wa kilogaramu limodzi pa mwanawankhosa aliyense.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo ndi anaankhosa asanu ndi awiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo pa mwana wankhosa aliyense mwa asanu ndi awiri aja, kilogalamu imodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
limodzi la magawo khumi likhale la mwana wa nkhosa mmodzi, momwemo ndi ana a nkhosa asanu ndi awiri;