Numbers 28:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwanawankhosa mmodzi muzimpereka m'maŵa, winayo muzimpereka madzulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwanawankhosa mmodziyo umpereke m'mawa, ndi mwanawankhosa winayo umpereke madzulo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa muzipereka mwana wankhosa mmodzi ndipo winayo madzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwana wa nkhosa mmodziyo umpereke m'mawa, ndi mwana wa nkhosa winayo umpereke madzulo;