Numbers 29:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pa tsiku lachisanu ndi chitatu muchite msonkhano waulemu. Musagwire ntchito zotopetsa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lachisanu ndi chitatu muzikhala nalo tsiku loletsa; musamachita ntchito ya masiku ena;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Pa tsiku lachisanu ndi chitatu muzichita msonkhano ndipo musamagwire ntchito iliyonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lacisanu ndi citatu muzikhala nalo tsiku loletsa; musamacita nchito ya masiku ena;