Numbers 29:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo mupereke chopereka cha chakudya chosakaniza ndi mafuta, wa makilogaramu atatu pa ng'ombe yamphongoyo, wa makilogaramu aŵiri pa nkhosa yamphongoyo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi nsembe yao ya ufa wosalala wosanganiza ndi mafuta, atatu a magawo khumi akhale a efa wa ng'ombe, awiri a magawo khumi akhale a nkhosa yamphongo imodziyo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa ngʼombe yayimuna iliyonse, muzikonza chopereka cha chakudya cha makilogalamu atatu a ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta; pa nkhosa yayimuna iliyonse makilogalamu awiri;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi nsembe yao ya ufa wosalala wosanganiza ndi mafuta, atatu a magawo khumi akhale a ng'ombe, awiri a magawo khumi akhale a nkhosa yamphongo imodziyo;