Numbers 3:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Umusankhe Aroni ndi ana ake, kuti azitumikira pa ntchito yaunsembe. Koma wina aliyense akayandikira pafupi, aphedwe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma uike Aroni ndi ana ake amuna, azisunga ntchito yao ya nsembe; ndi mlendo wakusendera pafupi amuphe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Usankhe Aaroni ndi ana ake aamuna kuti azitumikira pa ntchito ya unsembe. Koma wina aliyense woyandikira malo opatulika aphedwe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma uike Aroni ndi ana ace amuna, azisunga nchito yao ya nsembe; ndi mlendo wakusendera pafupi amuphe.