Numbers 3:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ana a Geresoni potsata mabanja ao naŵa: Labini ndi Simei.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Geresoni maina ao ndi awa, monga mwa mabanja ao: Libini, ndi Simei.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mayina a ana a Geresoni potsata mabanja awo ndi awa: Libini ndi Simei.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Gerisoni maina ao ndi awa, monga mwa mabanja ao: Libini, ndi Simei.