Numbers 3:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Alibini ndi Asimei anali mabanja otuluka mwa Geresoni. Ameneŵa ndiwo anali mabanja a Ageresoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Banja la Libini, ndi mabanja a Simei, ndiwo a Geresoni; ndiwo mabanja a Geresoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa Geresoni kunali banja la Alibini, banja la Asimei. Amenewa ndiwo anali mabanja a Ageresoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Banja la Libini, ndi mabanja a Simei, ndiwo a Gerisoni; ndiwo mabanja a Gerisoni.