Numbers 3:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mabanja a Geresoni ankamanga zithando zao kumbuyo kwa chihema cha Mulungu mbali yakuzambwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mabanja a Ageresoni azimanga mahema ao pambuyo pa Kachisi kumadzulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mabanja a Ageresoni azimanga misasa yawo kumadzulo, kumbuyo kwa Chihema.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mabanja a Agerisoni azimanga mahema ao pambuyo pa kacisi kumadzulo.