Numbers 3:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Eliyasafu mwana wa Laele ndiye anali mtsogoleri wa banja la makolo a Ageresoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kalonga wa nyumba ya makolo a Ageresoni ndiye Eliyasafu mwana wa Laele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtsogoleri wa mabanja a Ageresoni anali Eliyasafu mwana wa Laeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kalonga wa nyumba ya makolo a Agerisoni ndiye Eliyasafe mwana wa Layeli.