Numbers 3:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mabanja a ana a Kohati ankamanga zithando zao kumwera kwa chihema cha Mulungu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mabanja a ana a Kohati azimanga mahema ao pa mbali ya Kachisi ya kumwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mabanja a ana a Kohati ankamanga misasa yawo kummwera kwa Chihema.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mabanja a ana a Kohati azimanga mahema ao pa mbali ya kacisi ya kumwera.