Numbers 3:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamodzi ndi Elizafani, mwana wa Uziyele, amene anali mutu wa mabanja a Akohati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kalonga wa nyumba ya makolo ao ya mabanja a Akohati ndiye Elizafani mwana wa Uziyele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtsogoleri wa magulu a mabanja a Kohati anali Elizafani mwana wa Uzieli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kalonga wa nyumba ya makolo ao ya mabanja a Akohati ndiye Elizafana mwana wa Uziyeli.