Numbers 3:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chiŵerengero chao potsata kuchuluka kwa amuna onse, kuyambira mwana wamwamuna wa mwezi umodzi ndi wopitirirapo, chinali 6,200.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo owerengedwa ao, powerenga amuna onse, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu, ndiwo zikwi zisanu ndi chimodzi kudza mazana awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiwerengero cha amuna onse kuyambira a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 6,200.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo owerengedwa ao, powerenga amuna onse, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu, ndiwo zikwi zisanu ndi cimodzi kudza mazana awiri.