Numbers 3:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adauza Mose kuti, “Uŵerenge ana achisamba onse aamuna a Aisraele, kuyambira a mwezi umodzi ndi opitirirapo, potchula maina ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anati kwa Mose, Werenga amuna oyamba kubadwa onse a ana a Israele kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu nuone chiwerengo cha maina ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anawuza Mose kuti, “Werenga ana onse aamuna oyamba kubadwa mu Israeli, omwe ali ndi mwezi umodzi kapena kupitirirapo ndipo ulembe mndandanda wa mayina awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anati kwa Mose, Werenga amuna oyamba kubadwa onse a ana a Israyeli kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu nuone ciwerengo ca maina ao.