Numbers 30:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mkazi wokwatiwa akalonjeza nalumbira kuti adzachitadi zimene walonjeza,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ngati anawinda m'nyumba ya mwamuna wake, kapena anamanga moyo wake ndi chodziletsa ndi kulumbirapo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma ngati mayi wokwatiwa alumbira nalonjeza kuti adzachitadi zimene walonjeza,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ngati anawinda m'nyumba ya mwamuna wace, kapena anamanga moyo wace ndi codziletsa ndi kulumbirapo,