Numbers 30:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkazi akakhala mtsikana, nakhalabe m'nyumba ya bambo wake, ndipo alumbira kwa Chauta kuti adzachitadi zina zake zimene walumbira,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mkazi akachitira Yehova chowinda, nakadzimanga nacho chodziletsa, pokhala ali m'nyumba ya atate wake, m'unamwali;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pamene munthu wamkazi amene akukhalabe mʼnyumba ya abambo ake alumbira kwa Yehova kuti adzachita zimene walonjeza pa ubwana wake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mkazi akacitira Yehova cowinda, nakadzimanga naco codziletsa, pokhala ali m'nyumba ya atate wace, m'unamwali;