Numbers 30:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati mkazi alonjeza kapena alumbira mosaganiza bwino kuti adzachitadi kanthu kena, ndipo pambuyo pake akwatiwa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akakwatibwa naye mwamuna, pokhala ali nazo zowinda zake, kapena zonena zopanda pake za milomo yake, zimene anamanga nazo moyo wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati akwatiwa atalumbira kale kapena ngati alonjeza mofulumira ndi pakamwa pake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akakwatibwa naye mwamuna, pokhala ali nazo zowinda zace, kapena zonena zopanda pace za milomo yace, zimene anamanga nazo moyo wace;