Numbers 31:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose adaŵafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mwaŵasiya amoyo akazi onse?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose ananena nao, Kodi mwasunga ndi moyo akazi onse?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anafunsa kuti, “Kodi nʼchifukwa chiyani mwawaleka amoyo amayi onsewa?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose ananena nao, Kodi mwasunga ndi moyo akazi onse?