Numbers 31:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gawo la ankhondo amene adapita ku nkhondo linali nkhosa 337,500,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo limodzi la magawo awiri, ndilo gawo la iwo adatuluka kunkhondo, linafikira nkhosa zikwi mazana atatu mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gawo la ankhondo amene anapita ku nkhondo linali: nkhosa 337,500,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo limodzi la magawo awiri, ndilo gawo la iwo adaturuka kunkhondo, linafikira nkhosa zikwi mazana atatu mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu.