Numbers 31:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo gawo la Chauta linali nkhosa 675.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi msonkho wa Yehova wankhosa ndiwo mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi awiri mphambu zisanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mwa zimenezi gawo la Yehova linali 675;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi msonkho wa Yehova wankhosa ndiwo mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi awiri mphambu zisanu.