Numbers 31:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adauza Moseyo kuti, “Atumiki anufe taŵerenga ankhondo amene tikuŵalamulira, ndipo palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene akusoŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati kwa Mose, Atumiki anu anawerenga ankhondo tinali nao, ndipo sanasowe munthu mmodzi wa ife.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
iwo anati kwa iye, “Ife anthu anu tawerenga ankhondo amene timawalamulira. Palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene wasowa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati kwa Mose, Atumiki anu anawerenga ankhondo tinali nao, ndipo sanasowa munthu mmodzi wa ife.