Numbers 31:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapha mafumu a ku Midiyani pamodzi ndi anthu ao omwe. Mafumuwo anali Evi, Rekemu, Zuri, Huri ndi Reba, mafumu asanu a ku Midiyani. Adaphanso ndi lupanga Balamu mwana wa Beori.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapha mafumu a Amidiyani pamodzi ndi ophedwa ao ena; ndiwo Evi, ndi Rekemu, ndi Zuri, ndi Huri, ndi Reba, mafumu asanu a Amidiyani; namupha Balamu mwana wa Beori ndi lupanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa anthu ophedwawo munali Evi, Rekemu, Zuri, Huri ndi Reba, mafumu asanu a Amidiyani. Ndipo anaphanso ndi lupanga Balaamu mwana wa Beori.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapha mafumu a Amidyani pamodzi ndi ophedwa ao ena; ndiwo Evi, ndi Rekamu, ndi Zuri, ndi Huri, ndi Reba, mafumu asanu a Amidyani; namupha Balamu mwana wa Beori ndi lupanga.