Numbers 32:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibe ndi mmodzi yemwe amene adzaone dzikolo, kupatula Kalebe yekha mwana wa Yefune, Mkenizi uja, ndi Yoswa mwana wa Nuni, chifukwa iwoŵa ndiwo adatsata Chauta kwathunthu.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma Kalebe mwana wa Yefune, Mkenizi, ndi Yoswa mwana wa Nuni ndiwo; popeza anatsata Yehova ndi mtima wonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe ndi mmodzi yemwe kupatula Kalebe mwana wa Yefune, Mkeni, ndi Yoswa mwana wa Nuni chifukwa anatsatira Yehova ndi mtima wonse.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma Kalebi mwana wa Yefune, Mkenizi, ndi Yoswa mwana wa Nuni ndiwo; popeza anatsata Yehova ndi mtima wonse.