Numbers 32:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsopano inu mwaloŵa m'malo mwa makolo anu, inu mbadwo watsopano wa anthu ochimwa, ndipo mukufuna kuti muwonjezere mkwiyo woopsa wa Chauta pa Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo taonani, mwauka m'malo mwa makolo anu, gulu la anthu ochimwa, kuonjezanso mkwiyo waukali wa Yehova pa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndipo onani tsopano, inu mʼbado wochimwa, mwalowa mʼmalo mwa makolo anu ndipo mwachititsa kuti Yehova akwiyire Israeli kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo taonani, mwauka m'malo mwa makolo anu, gulu la anthu ocimwa, kuonjezanso mkwiyo waukali wa Yehova pa Israyeli,