Numbers 32:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mangani mizinda ya ana anu, ndi makola a nkhosa zanu, koma muchitedi zimene mwalonjeza.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dzimangireni midzi ya ana anu, ndi makola a zoweta zanu; ndipo muzichite zotuluka m'kamwa mwanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amangireni akazi ndi ana anu mizinda, mangani makola a ziweto zanu, koma chitani zomwe mwalonjeza.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dzimangireni midzi ya ana anu, ndi makola a zoweta zanu; ndipo muzicite zoturuka m'kamwa mwanu.