Numbers 32:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo zidzukulu za Gadi ndi za Rubeni zidayankha kuti, “Ife atumiki anu tidzachita zomwe Chauta watiwuza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Gadi ndi ana a Rubeni anayankha, nati, Monga Yehova anati kwa anyamata anu momwemo tidzachita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Agadi ndi Arubeni anayankha kuti, “Antchito anu adzachita zimene Yehova wanena.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Gadi ndi ana a Rubeni anayankha, nati, Monga Yehova anati kwa anyamata anu momwemo tidzacita.