Numbers 32:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Betenimira ndi Beteharani. Yonseyo inali yozingidwa ndi malinga. Ndipo adamanganso makola a nkhosa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Betenimura, ndi Beteharani: midzi ya m'malinga, ndi makola a zoweta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Beti-Nimira ndi Beti-Harani mizinda ya malinga. Anamanganso makola a ziweto zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Beti Nimira, ndi Beti Harani: midzi ya m'malinga, ndi makola a zoweta.