Numbers 32:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A fuko la Makiri, mwana wa Manase, adapita kukalanda dziko la Giliyadi napirikitsa Aamori amene ankakhala m'dzikomo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Makiri mwana wa Manase ananka ku Giliyadi, naulanda, napirikitsa Aamori anali m'mwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Makiri mwana wa Manase zinapita ku Giliyadi kulanda mzindawo ndi kuthamangitsira kunja Aamori omwe anali kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Makiri mwana wa Manase anamka ku Gileadi, naulanda, napitikitsa Aamori anali m'mwemo.