Numbers 32:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Makolo anu adachita zotero, pamene ndidaŵatuma kuchokera ku Kadesi-Baranea, kuti akaone dziko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anatero makolo anu, muja ndinawatumiza achoke ku Kadesi-Baranea kukaona dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Izi ndi zimene makolo anu anachita pamene ndinawatuma kuchokera ku Kadesi kukaona dzikolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anatero makolo anu, muja ndinawatumiza acoke ku Kadesi Barinea kukaona dziko.