Numbers 33:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanyamuka ku Elimu, nakamanga mahema ao m'mbali mwa Nyanja Yofiira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anachokera ku Elimu, nayenda namanga ku Nyanja Yofiira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atachoka ku Elimu anakamanga misasa yawo mʼmbali mwa Nyanja Yofiira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anacokera ku Elimu, nayenda namanga ku Nyanja Yofiira.