Numbers 33:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanyamuka ku Dofika, nakamanga mahema ao ku Alusi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nachokera ku Dofika, nayenda namanga m'Alusi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atachoka ku Dofika anakamanga misasa yawo ku Alusi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nacokera ku Dofika, nayenda namanga m'Alusi.