Numbers 33:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanyamuka ku Alusi, nakamanga mahema ao ku Refidimu kumene kunalibe madzi akumwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nachokera ku Alusi, nayenda namanga m'Refidimu; kumeneko kunalibe madzi kuti anthu amwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atachoka ku Alusi anakamanga misasa yawo ku Refidimu, kumene kunalibe madzi woti anthu ndi kumwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nacokera ku Alusi, nayenda namanga m'Refidimu; kumeneko kunalibe madzi kuti anthu amwe.