Numbers 33:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanyamuka ku Hazeroti, nakamanga mahema ao ku Ritima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nachokera ku Hazeroti, nayenda namanga m'Ritima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atachoka ku Heziroti anakamanga ku Ritima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nacokera ku Hazeroti, nayenda namanga m'Ritima.